Xander

Yemwe ndi Paul

Mwana wodzichepetsa komanso kwao ndi kwa chuma. Mu nkhani yake Xander akuonetsa kufunika kokhala ndi amnzako: ali ndi chifundo ndi amnzake, sasankha ocheza nae kaya wosauka chotani ngakhale wopata kumene.

“ Chomwe chinandidolola mtima ku Zathu ndi nyimbo komanso zisudzo. Ndili mwana ndinkalakalaka nditamapanga zimenezi, apatu ndie kuti maloto anga aphelezela chifukwa cha Zathu. Aka ndikoyamba Mmalawi muno kukhala ndi ganizo la pulogalamu ya atsikana ndi anyamata pamodzi kutukula dziko lino. Izi zipindulira anthu ambiri mdziko muno.” Paul

Share your feedback