Annetti

Yemwe ndi “Kas”

Ndi mtsikana koma zochitika ngati mnyamata. Amakhalira kugulitsa mayunitsi panseu. Kulimba mtima kwake komanso kusagonja kwawonetsa Annetti kuti ndizotheka munthu kuchita chomwe ukufuna pamoyo wako.

“Ndinkafunitsitsa kulembedwa ntchito ku Zathu chifukwa ndakhala ndikulakalaka mmoyo wanga kutukula achinyamata kudzela mu mnyimbo komanso zisudzo. Nduona kuti Zathu ili ndi kuthekela kopatsa achinyamata mwayi wolankhula zakukhosi zomwe sizinachitikeko mmbuyomu.” Kas

Share your feedback