Tiuzeni Nkhani Zanu

Tikufuna timve nkhani zanu....

Tikufuna timve nkhani zanu. Tiuzeni za nthawi imene munachita chinachake, kapena munapambana pachinthu chimene sichimayembekezeledwa chifukwa ndinu mnyamata olo mtsikana.

Mwina munathandiza mtsikana kunyamula madzi monga adachitira JP kwa Chikondi. Mwinanso ndinu mtsikana ndipo mukhumba kukhala wogwira ntchito za manja ngati Engeneer. Musachedwe, tiuzeni!

Mutha kulemba pa website pathu pompa mukalembetsa....

Share your feedback