Gogo

Yemwe ali mwini malangizo, alinso ndi nzeru zakuya komanso amadziwa zinthu zambiri. Iwo ndie mwini chikhalidwe. Ali ngati Namkungwi. Akuimila m’bado wozindikila wa-ankhala kale.

Gogo ndiyemwe achinyamata akutula nkhawa zawo. Aziyankha mafunso awo komanso kulunzanitsa m’bado waachinyamata ndi achikulile.

Share your feedback