Chikondi

Yemwe ndi Esther

Mwana wamasiye yemwe akukhala ndi Anti ake ovuta komanso iyeyu nthawi zambiri amanyentchera kulongosola zipsinjo zomwe akukumana nazo. Iyeyu zokhumba zake ndi zakuya ndipo akufunitsitsa atakhala oyimila anthu milandu ngati lawyer. Chikondi adolola anthu ena kukhala wodzikhulupilira.

“Chomwe chimandiwaza kwambiri kukhala mmodzi wa Zathu ndi chakuti sindigwira ntchito ndekha, palinso anthu ena ambiri ndi nkhani zawo zosiyanasiyana. Tonsefe tibweretsa kusintha padziko pano. Zathu ithandiza achinyamata kumasuka komanso kugwira ntchito limodzi potukula Malawi.” Esther

Share your feedback

Your thoughts

Robert

Ndi nyatwa

June 12, 2022, 10:12 a.m.