-
Mverani ndikupanga download nyimbo ya Zathu Band yatsopano...
Wonerani music video ya Zathu Band yoyamba....
Nyimbo yatsopano ndi video yake zikubwera pompano, muzaipeza pano kuyambira pa 24 July kupita mtsogolo.
Nayi kalawitsa wa nyimbo yatsopano ndi video yake.
Nyimbo yatsopano ndi video yake yotchedwa ‘Sitigonja’ kuchokera ku Zathu Band zili pano!
Video yonse ituluka pa 30 October!
Mverani ndikupanga download nyimbo ya Paga Zako kuchokera ku Zathu Band.
Zathu Band ikhala kutulutsa album yawo yoyamba yotchedwa "Chinzathu Ichichi" pa 19 February.