Mverani, Onerani ndi kupanga Download Sitigonja ya Zathu Band

Nyimbo yatsopano ndi video yake yotchedwa ‘Sitigonja’ kuchokera ku Zathu Band zili pano!

Nyimbo yatsopano ndi video yake yotchedwa ‘Sitigonja’ kuchokera ku Zathu Band zili pano! Atawina mpikisano wanyimbo mu video yawo yoyamba, ‘Zimatere Zimatere’; Xander, Chikondi, Annetti, Mphatso, T-Reel and JP apeza thandizo kuchokera kwa a Gogo, nkupita kukajambulitsa kuti akakhazikitse band yawo. Koma akudziwa malo okajambulitsilakowo? Kodi akafikako nthawi yabwino? Oyimba otchuka, Lulu, akupezekanso mu videoyi.

Mverani ndikupanga Download nyimbo ya Sitigonja pansipa:

Pa Free Basics Mverani ndikupanga download

Wonerani ndikupanga Download Sitigonja Video pansipa:

Tobwanyani apa kuti mupange download mwaulele

Share your feedback