Zathu Pa Wailesi. Series 1. Epidsode 12

Mwatumiza mauthenga anu kwa Gogo? Mverani ngati awulutsidwa. Ngati sanawulutsidwe tumizani uthenga pa SMS ku 0999 353535 kapena 0888 353535 kuti awulutse mtsogolomu

Pa Free Basics Listen and download

Mutha Kumvera uku:

MBC Radio 2 - Lolemba 15.30, Lachitatu 15.30, Loweluka 17.00

Zodiak - Lolemba 14:05, Lachisanu 15:30, Lamulungu 13:30

YONECO - Lachiwiri 16.30, Lachinayi 16.30, Loweluka 16.30

Voice of Livingstonia - Lachiwiri 16.30, Lachisanu 16.30, Loweluka 16.30

Share your feedback