Zathu pa wailesi Season 4 Episode 13

Mu sewelo latha tinaona Xander ndi Bambo ake anakwanitsa kumumangitsa Happy chifukwa cha milandu yake. Kodi umenewu ukhala mwai woti zinthu zibwelele momwe zinalili pakati pa Xander ndi abambo ake? Nanga kodi akuoneka okhumudwa chifukwa chani? Tiyeni timvele limodzi.....

Share your feedback