Zathu Pa Wailesi Season 2 ikubwera Posachedwa!

....kuyambira pa 11 November.

Season 2 ya Zathu Pa Wailesi ikubwera kuyambira pa 11th November. Tili ndi zatsopano mumagawo onse monga Timve Kwa Inu, kuyankha mafunso kwa Gogo, nyimbo, sewero ndi zambiri. Sungani tsiku limeneli.

Share your feedback