Mphatikizo wama pulogalamu, week yachisanu ndi chiwiri

Yikes, JP ndi Mphatso anyanyalitsana…mukufuna kudziwa zakhala bwanji? Pangani downloda mphatikizo wamapulogaramu amsabatayi.

Pa Free Basics Mverani ndikupanga download

Mutha Kumvera uku:

MBC Radio 2 - Lolemba 15.30, Lachitatu 15.30, Loweluka 17.00

Zodiak - Lolemba 14:05, Lachisanu 15:30, Lamulungu 13:30

YONECO - Lachiwiri 16.30, Lachinayi 16.30, Loweluka 16.30

Voice of Livingstonia - Lachiwiri 16.30, Lachisanu 16.30, Loweluka 16.30

Share your feedback