Mphatikizo wama pulogalamu, week ya chikhumi ndi chiwiri

Kwangosala ma show ochepa kukatha yalero. Kansakaniza wachikhumi ndi chiwiri wa Zathu pa Wailesi ali pano. Mverani ndikupangani download.

Pa Free Basics Mverani ndikupanga download

Mutha Kumvera uku:

MBC Radio 2 - Lolemba 15.30, Lachitatu 15.30, Loweluka 17.00

Zodiak - Lolemba 14:05, Lachisanu 15:30, Lamulungu 13:30

YONECO - Lachiwiri 16.30, Lachinayi 16.30, Loweluka 16.30

Voice of Livingstonia - Lachiwiri 16.30, Lachisanu 16.30, Loweluka 16.30

Share your feedback