Mphatikizo wama pulogalamu, week yachikhumi

Tcherani kuti mumve kulinji M'Malawi muno mu 'Timve Kwa Inu', mverani nyimbo zodolola mtima za Zathu Band komanso oimba ena otchuka. Mverani kuti kodi anthu amusewero lathu zikuwayendera bwanji popanga download kapena pomvetsera show yatsopano pompano.

Pa Free Basics Mverani ndikupanga download

Mutha Kumvera uku:

MBC Radio 2 - Lolemba 15.30, Lachitatu 15.30, Loweluka 17.00

Zodiak - Lolemba 14:05, Lachisanu 15:30, Lamulungu 13:30

YONECO - Lachiwiri 16.30, Lachinayi 16.30, Loweluka 16.30

Voice of Livingstonia - Lachiwiri 16.30, Lachisanu 16.30, Loweluka 16.30

Share your feedback