Zathu Band yatulutsa album yatsopano

Zathu Band yatulutsa chi album chatsopano! kuonjezela pa nyimbo zitatu zoyambilila zija, Zathu Band yabwela ndi nyimbo zina zisanu ndi ziwili, kuphatikizapo zimenezi mu album yi muli interview ya Zathu Band akufotokoza ambili zokhudza album yawo. Mveran imodzi mwa nyimbo zawo yotchedwa 'Malawi pansipa...

Pa Free Basics Mveran ndi kupanga download

Onerani ndi Kupanga download

Pangani download apa

mutha kumvera uku:

MBC Radio 2 - Lolemba 15.30, Lachitatu 15.30, Loweluka 17.00

Zodiak - Lolemba 14:05, Lachisanu 15:30, Lamulungu 13:30

YONECO - Lachiwiri 16.30, Lachinayi 16.30, Loweluka 16.30

Voice of Livingstonia - Lachiwiri 16.30, Lachisanu 16.30, Loweluka 16.30

Share your feedback