Okondeka agogo, ine ndakwanitsa zaka 13 koma sindinayambe kusamba. Ndiyembekezele masiku ake ati akuti ndithe nsinkhu?

Usadandaule, palibe chomwe ungachite kuti uthe nsinkhu. Nthawi ikwana yokha pakali pano ukanalibe wachichepele. Komabe suuli patali ukwanitsa pompano. Zaka zake ndipakati pa 12 ndi 18.

Izi zikutantahuza kuti pali ena amatha nsinkhu asanakwane zaka 12 mwinanso ena mpaka zaka kupitilira 18. Izi zimachitika osadandaula.

Share your feedback