Season 3 Episode 1

Season 3 yayamba! Tiyeni tione zomwe Xander, Annetti, Chikondi, Mphatso, T-Reel komanso JP akhale akuchita mu season 3, pamene C-Zee ndi Goxy akutipatsila nyimbo, komanso kucheza ndi alendo osiyanasiyana mu Timve Kwa Inu. Sangalalani!

Share your feedback