Zathu Band's Zimatere Zimatere Lyrics

Check out our Song lyrics for the firt single, written by Faith Mussa.

1st Verse

Ndukufuna anzanga ocheza nawo / Oseka nawo / But where is everyone when I need them the most Ndikufuna anzanga/ I am searching now Tidzithandizana/

*1st Verse Rap *

Sister osadanda / Nje usaope, tapachika mantha/ Ndipatse nkono ndikugwire dzanja / Ndiwe nzanga, Am your brother / Ndikuthandiza ngini tipanga nde../ he! wationa bwanji/ Ah iwe ndi ine patali/ kugwila ntchito limodzi/ Sangamake tiye tichinye zigoli/

Chorus

Zimatere Zimatere / If things could be like this (Malawi Proverb) Tere tere tere Bwenzi zikoma/ It would be amazing, amazing. (Malawi Proverb) Koma koma koma Mwationa bra / Look us at now Mwationa bwa, Mwationa bwa / Look at us at now, Look at us now. Chilling together Tikuoneka bwa / How do we look, How do we look Friends forever

*2nd Verse *

Poti mutu umodzi susenza denga/ Because one head can not carry a roof Timagwirana dzanja wina akagwa/ We should hold each others hand when on falls Khalidwe lathu lopereka chitsanzo/ Our character is exceptional ! We are friends for life and we love it that way!

2nd Verse

tcha tcha tatiyeko tisewele phada / cha cha, lets go play ‘phada’ Chipapa tiombeko mmanja/ ‘Chipapapa’ clap your hands Ndikukankha ukatopa / I lift when you are tired ukangogwa ndikutola / When you fall I will pick you up Pali awili palibepo mantha / When we’re together there is no fear Chako ndi changa / What’s yours is mine Micasa sucassa / What’s mine is yours Apo ndi apa / Come close, don’t be afraid Mtsikana suntha apa / Let’s move in rhythm Chako ndi changa / What’s yours is mine Micasa sucassa / What’s mine is yours Tipange mwa choncho tiye chotsa mantha

Chorus

(Call) Zimatere Zimatere / If things could be like this. (Malawi Proverb) (Response) Bwenzi zikoma / It would be amazing, amazing. (Malawi Proverb) (Call) Mwationa bra, Mwationa bra / Look us at now (Response) Mwationa bra, Mwationa bra / At us at now, at us now. (Call) Chilling together (Response) Tikuoneka bwa / How do we look?, How do we look? Friends forever

Bridge

Ife tonse, we can do anything / All of us, we can do anything If we put our hearts into in Tiyende limodzi, tigwilane manja / Lets move together, lets hold each others hands Tonse tiqwilizane / We should be united Ngati (Nthabwala) x 4 / Its a joke x 4 ??? Tikaona zikutheka palimodzi / We will see things happen Zingofunana khama lanthu / We just need hard work Kulimbika kwathu / and perseverance ndimtima wachikondi / and hearts full of love

Share your feedback