Season 6 ya Zathu Pa Wailesi yayamba. Pitilizani kutsatila mmene miyoyo ya achinyamata a Zathu Band ikhale ikuyendela mu Seasoniyi, komanso tili ndi mpikisano wosangalatsa kwambili, wosavuta kuutsatila ndipo chofunika ndikungomvera ma episode a Season 6 kuti mudziwe zoyenela kuchita.
Share your feedback