• English
  • Menu

Za Zathu

Zathu ndi pulogalamu yokhayo ya achinyamata makamaka achisodzela muno M’malawi. Timakupatsilani pulogalamuyi pawayilesi kawiri sabata iliyonse momwe tili ndi sewero lokamba za mayesero ndi mavuto achinyamata, yopangingwanso ndi achimata eniake. Palinso Nyimbo zapamwamba za Zathu Band, komanso macelebu ena.

Tilinso ndi Talk Show yomwe azikupatsilani ndi Lily B ndi DJ Goxy. Mmenemu mukhala ndi mpata wofunsa mafunso komanso kumva malangizo kuchokela kwa Gogo ndi akatswiri ena M’malawi muno. Timajambula Nyimbo zakanema zapamwamba zojambulidwa bwino ndi a Zathu Band zomwe mutha kupanga download mwaulere:

Nkhani Zathu. Nyimbo Zathu. Moyo Wathu.

Mverani Sabata Iliyonse Pa:

MBC Radio 2 - Lolemba 15.30, Lachitatu 15.30, Loweluka 17.00

Zodiak - Lolemba 14:05, Lachisanu 15:30, Lamulungu 13:30

YONECO - Lachiwiri 16.30, Lachinayi 16.30, Loweluka 16.30

Voice of Livingstonia - Lachiwiri 16.30, Lachisanu 16.30, Loweluka 16.30

  • Facebook Zathu Pa Wailesi
  • Home
  • Nkhani Zathu
  • Show Yathu
  • Nyimbo Zathu
  • Moyo Wathu
  • Za Zathu
  • Kagwiritsidwe ntchito kake
  • Keyala
  • Ndondomeko ya Malamulo

© 2025 Zathu. All Rights Reserved.