English Chichewa
Menu Sign up Search
Our Show
Zathu Pa Wailesi Season 2

Zathu Pa Wailesi Season 2 yayamba!

Mverani ku ma episode anyuwani week iliyonse...

Read more

Zathu Pa Wailesi Season 2 yayamba ndi ma episode okoma. Tili ndi show yobeba m'mene muli Timve Kwa Inu, Sewero, mafunso ndi mayankho a Gogo, ndi nyimbo zabwino.

Mutha Kumvera uku:

MBC Radio 2 - Lolemba 15.30, Lachitatu 15.30, Loweluka 17.00

Zodiak - Lolemba 14:05, Lachisanu 15:30, Lamulungu 13:30

YONECO - Lachiwiri 16.30, Lachinayi 16.30, Loweluka 16.30

Voice of Livingstonia - Lachiwiri 16.30, Lachisanu 16.30, Loweluka 16.30

Back to Top