JP

Yemwe ndi Joe

Mwana wakhama yemwe kholo lake ndi refuji, anachokela ku dziko la Congo ndipo akukhazikika kumene Mmalawi muno. Iyeyu ndi munthu wabwino, amacheza ndi aliyense komanso ndi mnzake kwambiri wa Chikondi. Mu mseweromu akuonetsa kufunikila kokhala ndi amnzako komanso ubwino wonena chilungamo chomwe iwe uli.

“Ineyo ndinafunsila ntchito ku Zathu chifukwa choti ndimafuna kugwiritsa ntchito luso langa posintha zinthu Mmalawi muno. Nduona ngati Zathu ithandiza achinyamata kugwira ntchito limodzi posaona kusiyana kwao.” Joe

Share your feedback