Zathu Pa Wailesi Season 4 Episode 6

DJ Goxy ndi C-Zee akusungilani list ya nyimbo zosangalatsa mu episodi iyi, Gogo akhala akukuyankhani mafunso omwe munawafunsa komanso khalani tcheru kuti mumvetsere kuti kodi T-Reel, Mphatso ndi Chikondi apanga chisankho chotani poti JP anawauza kuti asankhe pakati pa iyeyo ndi Xander? Mvetselani....................

Share your feedback