Zathu Pa Wailesi. Season 1. Epidsode 17

Mafunso okondweretsa kuchokera kwa Gogo lero. Mverani m'mene anayankhira limodzi mwamafunso amene m'modzi wa omvera athu afunsa molingana ndi m'dulidwe wa amuna ndi matenda a Edzi.

Share your feedback