Mphatikizo wama pulogalamu, week yachisanu ndi chitatu

Mafunso opatsa chidwi kuchokela kwa omvera pulogalamu ya Zathu kupita kwa Gogo alipo. Lero kulinso funso lochokera kwa Felistus amene ali mzimayi wachisikana, pangani download mphatikizo wamapulogalamu lero kuti mumve mulinji.

Pa Free Basics Mverani ndikupanga download

Mutha Kumvera uku:

MBC Radio 2 - Lolemba 15.30, Lachitatu 15.30, Loweluka 17.00

Zodiak - Lolemba 14:05, Lachisanu 15:30, Lamulungu 13:30

YONECO - Lachiwiri 16.30, Lachinayi 16.30, Loweluka 16.30

Voice of Livingstonia - Lachiwiri 16.30, Lachisanu 16.30, Loweluka 16.30

Share your feedback