Ndine mnyamata wazaka 15 ndimakonda kugwira ntchito ndi kuthandiza zapakhomo koma anthu amandiseka kuti ntchitozi sizoyenera kugwilidwa ndi munthu wam'muna. Izi ndi zoona?

Ndichinthu chopatsa chidwi kuti umathanso kuthandiza kugwila ntchito zapakhomo. Amati zonenena kupweteketsa mutu cholakwika ndichani kuti mwamuna agwire ntchito zapakhomo nanji kuthandiza abale okondeka.

Kale ndili mwana ntchito zambiri amagwira ndiatsikana koma masiku ano mnyamata kaya ndi mtsikana onse amagwira ntchito zapakhomo.

Share your feedback